Gulu la amayi la Kawalika Mother Care Group (MCG), layamikila ntchito yomwe bungwe la Malawi Health Equity Network (MHEN) likugwila pophunzitsa za kufunika kwa akatemela osiyanasiyana omwe ana osapyola dzaka zisanu amayenela kulandila, ponena kuti izi zachepetsa imfa za ana achichepele-wa. Wapampando wa gulu la amayi-wa Judith Nowa wanena izi pambuyo pa maphunzilo achibweleza (refresher […]
The post MHEN ayiyamikila pa ntchito yopititsa pa tsogolo nkhani za umoyo appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.