Mtsogoleri wa gulu la Citizens For Transformation (CFT), a Timothy Mtambo ati ndiokonzeka kugwilira ntchito limodzi ndi Democratic Progressive Party (DPP), chipani chimene anatengapo gawo kuti chichoke mu ulamuliro wa dziko la Malawi mu chaka cha 2019. A Mtambo amayankhula izi pa wayilesi ya Zodiak mu pologalamu ya padera yomwe yaulutsidwa Lachiwiri pa 7 May, […]
The post Mgwirizano ndi DPP ndiotheka- Mtambo appeared first on Malawi 24.