Aphungu a chipani cha UTM agawanikana mmene akufunira kukagwira ntchito mnyumba ya malamulo nkumano ukayambaika. Ena akuti sakufuna kukakhala mbali ya boma pomwe ena anenetsa kuti sachoka mbali ya boma. Mtsogoleri wa aphunguwa mnyumbayi a Chrissie Kanyasho wanena kuti alembera kalata Sipikala wa nyumba ya malamulo a Catherine Gotani Hara kuwadziwitsa za ganizo lawo. […]
The post Mgawaniko walowa ku aphungu a UTM: Ena akuti akhala kumbali ya boma, ena akuti ayi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.