Mfumu yaikulu Kachenga yamwalira

Mfumu yaikulu Kachenga ya m’boma la Balaka yamwalira. Bwanamkubwa wa boma la Balaka a Tamanya Harawa ndiwo atsimikiza izi mu kalata yomwe asainira. A Harawa ati mfumu Kachenga yamwalira lero masana akulandira chithandizo cha mankhwala pa chipatala cha Zomba Central. Mwambo oika m’manda thupi la  malemu  Kachenga, omwe dzina lawo ndi Mary Saidi, ulengezedwabe. Anabadwa […]

The post Mfumu yaikulu Kachenga yamwalira appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください