MEC yati anthu omwe ali ku Israel komanso mayiko ena akunja sadzakhala ndi mwayi oponya mavoti

Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno, la Malawi Electoral Commission (MEC) lati anthu omwe ali ku Israel komanso mayiko ena akunja sadzakhala nawo mwayi oponya mavoti pa zisankho za patatu zomwe zidzachitike m’mwezi wa September chaka cha 2025. Malingana ndi mneneri wa bungweli, a Sangwani Mwafulirwa, malamulo a dziko lino salola anthu omwe ali kunja kwa […]

The post MEC yati anthu omwe ali ku Israel komanso mayiko ena akunja sadzakhala ndi mwayi oponya mavoti appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください