Mchitidwe wa kadzanja ukuchedwetsa ntchito yokonzaso njanji ya Limbe-Sandama

Namondwe wa Freddy komanso mchitidwe okuba zichitsulo cha njanji ndi zina mwa zomwe zachedwetsa ntchito yokonzaso njanji  ya makilomita 72 ya Limbe-Sandama. Nduna yoyang’anira mayendwe komaso ntchito, Jocobo Hara, wati pakadali pano sizikudziwika nthawi yeniyeni imene ntchito yi idzamalizidwe chifukwa  contilakitala sakugwira  ntchitoyi. A Hara anauluraso kuti namondwe anaononga milatho yambiri imene imalumikiza njanjiyi komaso […]

The post Mchitidwe wa kadzanja ukuchedwetsa ntchito yokonzaso njanji ya Limbe-Sandama appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください