Mchitidwe osiya kumwa mankhwala a khate ukuchulukira — atero azaumoyo

Mchitidwe osiyira panjira kumwa mankhwala a matenda a khate m’boma la Balaka waoneka kuti ukuchulukira zomwe zikupangitsa kuti odwala nthendayi asamachire nsanga. Izi zadziwika pamene mkulu owona matenda apakhungu komanso a khate pa chipatala cha Balaka Alexander Memayako wauza atolakhani lachitatu kuti anthu omwe anapezeka ndi nthendayi akangowona kuti ayamba kuchira amasiya kumwa mankhwala zomwe […]

The post Mchitidwe osiya kumwa mankhwala a khate ukuchulukira — atero azaumoyo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください