Pamene maiko ochuluka amakumbukira tsiku la nyama ya Ngaka (pangolin) dzulo pa 17 February, akuluakulu oyang’anira nkhalango yotetezedwa ya Liwonde m’boma la Machinga ati mchitidwe ogwira ndi kuzembetsa nyamayi wachepa ku nkhalangoyi. Mkulu oyang’anira nkhalangoyi Mathias Kachepa Elisa wati ngankhale palibe chiwerengero chenicheni cha milandu yozembetsa Ngaka, anthu ambiri amene amakhudzidwa ndi milanduyi amagwiritsa ntchito […]
The post Mchitidwe okuba ndi kuzembetsa Pangolin wachepa mu nkhalango ya Liwonde appeared first on Malawi 24.