Anthu ena akwiya ndipo akulavulira za m’kamwa m’busa Yasin Gama kaamba ka ulaliki omwe amadzudzula anthu omwe amabwera ndi zinthu monga mabigili otungira madzi akapita m’dziko la South Africa. Lolemba sabata ino, a Gama omwe amapempheletsa pa mpingo wa Mvama CCAP ku Lilongwe, pansi pa sinodi ya Nkhoma, amachititsa mapemphero amadzulo pamutu oti ‘masomphenya’. M’kulalikira […]
The post M’busa Yasin Gama ‘akugendedwa’ polalikira za omwe amabwera ndi mabigili pochoka ku South Africa appeared first on Malawi24.