Kulibe kupuma ku Malawi; ina ikamatuluka, ina imakhala ikulowa, nkhani sizimatha. M’busa wina uku akuyenda chewu chewu kaamba koganizilidwa kuti wakhala akuchita kusaweluzika ndi mkazi wa nkhosa yake yomweso yakhala ikumupatsa chithandizo chochuluka, inde kuluma chala chokudyetsa phalacho. Nkhaniyi yayambira kutsamba la nchezo la thwita (twitter) komwe tsamba la ‘Accused Number One’ lasindikiza uthenga odandaula […]
The post M’busa ‘wadya’ nkhosa, mwini nkhosa wanyangala appeared first on Malawi24.