Mboni zisanu zambali ya Boma zatsiliza kuperekera umboni pamulandu wamkulu wa Bungwe la Malawi First a Bon Kalindo omwe akuwayimba mulandu owaganizira kuti adayambitsa zipolowe potsatira ziwonetsero zomwe adachititsa pa 23 November mu mzinda wa Zomba. Zina mwambonizo ndi apolisi anayi omwe ndi Stella Likukuta, Harry Dongolosi, Inspector Gauti, komanso Assistant Superintendent Isaac Mdala. Onsewa […]
The post Mboni zambali ya Boma zatsiliza kuperekera umboni pamulandu wa a Bon Kalindo appeared first on Malawi 24.