Njonda zitatu zomwe zidanjatidwa pa mlandu okuba katundu zitavala ngati gulewamkulu kwa Chaima m’boma la Kasungu azipeza zolakwa pa mlandu wakuba ndipo azilamula kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka 12. Nkhani yonse ikuti njondazi zitatuzi zomwe ndi a Sadarack Phiri azaka 48 zakubadwa, a Lazaro Nkhoma azaka 47 ndi a John Mkula azaka 35 […]
The post Mbava zitatu zomwe zimaba pobisalira gulewamkulu azilamula kukaseweza jere appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 