Anthu ena omwe sakudziwika mpaka pano akuti usiku wapitawu anakadawira galimoto ya boma ndikuba katundu wina wakunyumba yachifumu koma kwa pano akuti chinsalu chofiyira chija amayendapo mtsogoleri wa dziko m’misonkhano chija, chapezeka kutchile lina. Usiku wa Lachitatu pa 24 January, 2024 anthu ena omwe akuganizilidwa kuti ndi okuba, anakadamira galimoto ya Ku nyumba ya chifumu […]
The post Mbava zaba “carpet”, “tent” za mtsogoleri wa dziko appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
