Agenda ku polisi chamba chili mthumba: Abambo awiri a m’boma la Mwanza athilidwa zingwe powaganizira kuti ndi omwe anakadawira galimoto ya boma ikuyenda ndikuba tenti komaso chinsalu chofiyira chija amayendapo mtsogoleri wa dziko m’misonkhano chija. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani za polisi mdziko muno a Peter Kalaya omwe kudzera mu kalata yomwe yatulutsidwa masana […]
The post Mbava za kapeti, tenti ya mtsogoleri wa dziko zagwidwa appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
