Mayi wophwanya paipi yamadzi kuti atunge aulele walipira chindapusa cha K300,000

Mayi wa zaka 21 yemwe anamangidwa mkati mwa sabatayi chifukwa chophwanya mwadala paipi ya madzi a Blantyre Water Board ndicholinga choti atunge madzi aulele, amulipitsa chindapusa cha ndalama yokwana K300,000. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe a Aubrey Singanyama, a Celina Ganya omwe akuti anapalamula mlanduwu Lachiwiri sabata ino pa 5 March, 2024 […]

The post Mayi wophwanya paipi yamadzi kuti atunge aulele walipira chindapusa cha K300,000 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください