Mayi wina wasiya mwana wongobadwa kumene pa chipata cholowera pa chipatala chachikulu cha boma la Salima mbandakucha wa lero. Mneneri wa a polisi m’boma la Salima a Rabecca Ndiwate wati apolisi Apolisi ku Salima akufunafuna mayiyu. A Ndiwate ati mlonda yemwe amgwira ntchito ya usiku pachipatapo anamva mwana akulira chapafupi ndi pomwe iye anali ndipo […]
The post Mayi wasiya mwana obadwa kumene pa chipatala cha Salima appeared first on Malawi 24.