Mayi wazaka 38 yemwe dzina lake ndi Takondwa Banda ali m’manja mwa a polisi ku Kasungu kogwirira mwana wammuna wazaka 16 ndi kumupatsila matenda opatsilana pogonana. Mneneri wa polisi ya Kasungu Joseph Kachikho wati izi zinachitika mu mwezi wa Okotabala chaka chino. A Kachikho ati mnyamatayu analembedwa ntchito yogwira kumunda kwa a Banda ndipo amagona […]
The post Mayi wamangidwa kamba kogwilirira mwana wazaka 16 appeared first on Malawi 24.