Bwalo la milandu ku Dowa lagamula mayi wa zaka 42, Flora Thom, kukakhala ku ndende kwa chaka ndi miyezi itatu chifukwa chakuba katundu wa m’nyumba ya bwana wake wa ndalama pafupifupi K2 miliyoni. Bwaloli linamva kuchokera kwa oyimira boma pamlanduwu, Sub Inspector Patrick Mandanda kuti pa 6 August 2023, a Thom anaba katunduyu pomwe abwana […]
The post Mayi osamutsa katundu wa m’nyumba amugamula kukakhala ku ndende chaka chimodzi appeared first on Malawi24.