Mayi athawa atapha mamuna wake pomukoka katundu

Mayi wina yemwe dzina lake silikudziwika Boma la Zomba wathawa atapha mamuna wake pomukoka malo obisika. Wofalitsa nkhani za apolisi Boma la Zomba, Sub Inspector Patricia Sipiliano watsimikidza zankhaniyi poyankhula ndi Malawi24. Sub Inspector Sipiliano wati izi zachitika mmudzi mwa Makanjira mdera ya Mfumu yayikulu Chikowi Boma la Zomba ndipo wati  bamboyu dzina lake ndi […]

The post Mayi athawa atapha mamuna wake pomukoka katundu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください