Zina ukamva ndithudi kamba anga mwala; pamene inu mumasamba thukuta mukangophika chipagala kwa kanthawi kochepa, mayi wina ku Nigeria walowa mu tsiku lachitatu akuphika zakudya zosiyanasiyana osapuma. Hilda Effiong Bassey amene amadziwika kwambiri ndi dzina loti Hilda Baci, ochokela mdera la Akwa Ibom, mdziko la Nigeria, ndikatswiri pankhani za maphikidwe, ndipo atha kukuphikirani mwala inu […]
The post Mayi akuphika kwa masiku anayi osapuma appeared first on Malawi24.