Maumboni ambiri akupelekedwa: Maranatha ikuyambiraso ma adiveti

Patadutsa miyezi iwiri anthu atawasowa ma adiveti okhudza mankhwala azitsamba osiyanasiyana omwe samasempha nyumba yofalitsira mawu, kampani ya Maranatha yati yayambilaso kusatsa malonda ake munjira zonse. Bungwe loyang’anira za mankhwala la PMRA komaso loyang’anira ntchito yofalitsa mawu la MACRA, posachedwapa anaika ndondomekoyi ndicholinga chofuna kuonetsetsa kuti anthu akulandira mauthenga oyenera okhudzana ndi mankhwala m’dziko muno. […]

The post Maumboni ambiri akupelekedwa: Maranatha ikuyambiraso ma adiveti appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください