Yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) ku chigawo cha ku m’mawa a Hashim Banda ati masomphenya a chipani cha United Transformation Movement (UTM) anawakopa ndi chifukwa alowa chipanichi. Poyankhula pa msonkhano wa ndale omwe chipanichi chinapangitsa pa bwalo la Chinamwali ku Zomba a Banda ati nzosabisa kuti dziko likuyenera […]
The post Masomphenya a UTM ndi amphamvu, anandikopa – Hashim Banda appeared first on Malawi 24.