Kampani ya MultiChoice yatsimikizira anthu okonda masewero a mpira mdziko muno kuti mpira wa chaka chino wa Africa Cup of Nations (AFCON) ukhala ukuonetsedwa pa kanema wa Super Sport Chikalatachi chadza pamene masiku apitawo panali nkhawa yoti SuperSport sionetsa masewelowa pakanemayu. Ndipo malingana ndi kalata yomwe kampaniyi yatulutsa, masewera onse okwana 52 akhala akuonetsedwa pa […]
The post Masewero a AFCON awonetsedwa pa kanema wa SuperSport appeared first on Malawi 24.