Yemwe wangosankhidwa kumene kukhala mtsogoleri wa aphungu otsutsa boma wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) m’nyumba yamalamulo, mayi Mary Navicha akana kulankhulapo m’nyumbayi pa zomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera analankhula pomwe amatsekulira mkumano wa aphungu m’nyumbayi lachisanu. Sipikala wanyumbayi a Catherine Gotani Hara anapeleka mwayi kwa a Navitcha womwe akudziwika m’nyumbayi ngati mtsogoleri wa […]
The post Mary Navicha akana kuyankha za SONA mnyumba ya malamulo appeared first on Malawi 24.