Marinica wachenjeza a Malawi kuti asayembekezere zambiri ku COSAFA

Mphunzitsi wa Flames Mario Marinica wachenjeza a Malawi okonda mpira kuti asakhale ndi chiyembekezo chachikulu pomwe Flames ikhale ikukapikisana nawo mu mpikisano wa COSAFA wa chaka chino komwe ili mu gulu limodzi ndi Lesotho, Mauritius komanso Eswatini. Timu yomwe ikhale pamwamba mu gululi izakumana ndi Senegal yomwe ibwere ngati alendo ku mpikisanowu mu ndime ya […]

The post Marinica wachenjeza a Malawi kuti asayembekezere zambiri ku COSAFA appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です