Zachitikanso lero mumpingo wakatolika ku Lunzu pamene wansembe wathira bakera kukamwa oyambitsa kwaya kamba koyambitsa nyimbo ya Aleluya mu nyengo ino ya lenti mpaka mapemphero kusokonekera. Nkhani yonse ikuti a Edward omwe ndi oyambitsa kwaya amene amenyedwawa anayambitsa nyimbo panthawi yopereka mphatso ndipo nyimbo ili mkati panadzamveka mawu oti Aleluya. Apa wansembeyo anadzambatuka ndikukathira bakera […]
The post Mapemphero anasokonekera ku Lunzu wansembe atathira bakera kwaya masitala appeared first on Malawi 24.