Mavuta akuwoneka kuti sakutha ku nthambi yowona za anthu olowa ndi kutuluka m’dziko muno (immigration) pomwe nthambiyi yati ikukanika kutulutsa ziphaso zoyendera (Passport). Izi ndi malingana ndi uthenga wa nthambiyi kupita kwa a Malawi wati. “Tikuziwitsa a Malawi kuti makina athu wotulutsira ziphatso zoyendera (Passport) ali ndivuto ndipo pakadali pano sitikutulutsa ziphasozi koma anthu athu […]
The post Mapasipoti akukanika kutuluka ku Immigration appeared first on Malawi 24.