Pamene zinthu zikuvuta kale, anthu m’dziko muno ayembekeze kuti zinthu zitha kufika pothina zedi kamba koti ndalama ya kwacha yachepetsedwa mphamvu kuyelekeza ndi ndalama ya dollar ya ku America. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe banki yayikulu m’dziko muno ya Reserve (RBM) yatulutsa lachitatu pa 8 November, 2023 chomwe chasainidwa ndi gavanala wake a Wilson […]
The post Mangani malamba: Kwacha yachepetsedwa mphamvu appeared first on Malawi 24.