Timu ya mpira wa manja ya Malawi yasambwadza timu ya dziko la Fiji ndi zigoli 62 kwa 48 mu mpikisano wa dziko lonse la pansi wa Vitality Netball World Cup ku South Africa. Awa anali masewera oyamba mu ndime yachiwiri ya mpikisanowu ndipo anachitikira pa bwalo la Cape Town International Convention Centre lero. Malawi yomwe […]
The post Malawi yaphwasamula Fiji appeared first on Malawi24.