Malawi yapeza US$2m kuchokera ku Israel

Dziko la Malawi lapeza ndalama zokwana US$2 miliyoni (pafupipafupi 3.4 biliyoni Malawi Kwacha) kuchokera ku dziko la Israel kudzera mwa nzika za dziko lino zimene zikugwira ntchito m’dzikolo. Malinga ndi nduna ya zachuma a Simplex Chithyola, ndalamazi zakwera kuchoka pomwe zinali pa US$735,000 mu  mwezi wa February. Ndunayi inaonjezera kunena kuti ndalamazi zikumafikila mu ma […]

The post Malawi yapeza US$2m kuchokera ku Israel appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください