Mwambo okumbukira asilikali omwe adamenya nkhondo ya dziko lonse lapansi udachitika lero ku chipilala chachikumbutso ku Cobbe Barracks ku Zomba. Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino a Saulos Chilima ndi yemwe adatsogolera mtundu wa a Malawi panwambowo. A Chilima adafika kumwambowo pomwe nthawi imangokwana 10:58 mamawa ndipo adayala nkhata yamaluwa pachipilala chachikumbutsochocho. Kuno ku Malawi mwambowu […]
The post Malawi yakumbukira asilikali omwe adamenya nawo nkhondo za dziko lapansi appeared first on Malawi 24.