Malawi sakukwanitsa kusamalira atsogoleri ake akale – atero a Bakili Muluzi

Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi ati chisamaliro cha atsogoleri opuma chomwe boma limapereka  chikufunika  kuunikidwanso, ponena kuti pali zigwelu zambiri zofunika kukonza . Mtsogoleri wakaleyu wati, mwa chitsanzo, pakali pano amagwiritsa ntchito ndalama za mthumba mwake kugulira zakudya komanso mafuta a galimoto. A Muluzi ati adalankhulapo ndi mlembi wamkulu wa boma, a […]

The post Malawi sakukwanitsa kusamalira atsogoleri ake akale – atero a Bakili Muluzi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください