Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi ati chisamaliro cha atsogoleri opuma chomwe boma limapereka chikufunika kuunikidwanso, ponena kuti pali zigwelu zambiri zofunika kukonza . Mtsogoleri wakaleyu wati, mwa chitsanzo, pakali pano amagwiritsa ntchito ndalama za mthumba mwake kugulira zakudya komanso mafuta a galimoto. A Muluzi ati adalankhulapo ndi mlembi wamkulu wa boma, a […]
The post Malawi sakukwanitsa kusamalira atsogoleri ake akale – atero a Bakili Muluzi appeared first on Malawi 24.