Malawi Queens ili pa chiopsezo chosatenga nawo mbali mu mipikisano ina ya dziko lonse lapansi

Timu ya mpira wa manja ya dziko lino, Malawi Queens, ili pa chiopsenzo chosatenga nawo mbali mu mipikisano ina ikuluikulu ya dziko lonse lapansi monga Fast 5 Netball World Series yomwe imaseweredwa ndi matimu 6 omwe akuchita bwino pa dziko lonse. Queens padakali pano yatsika pa m’ndandanda wa matimu omwe akuchita bwino pa dziko lonse […]

The post Malawi Queens ili pa chiopsezo chosatenga nawo mbali mu mipikisano ina ya dziko lonse lapansi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください