Dorothy Kingston wadandaula zakhalidwe lomwe achita akuluakulu a Malawi Revenue Authority (MRA) komaso apolisi munzinda wa Lilongwe omwe akuti awazunza komaso kumumenya woyimba wachikulire Jetu. Dorothy yemwe ndi nkazi wake wa woyimba Zeze Kingston, wati gogo wa zaka 72-yu pamodzi ndi iye akumana ndi tsokali Lachinayi madzulo pomwe amabwelera ku Blantyre kuchokera ku Lilongwe komwe […]
The post Makosana a MRA abilibinya Jetu – Dorothy Kingston appeared first on Malawi 24.