Bungwe la Civil Society Advocacy Forum on HIV and Related Conditions (CSAF) lati pakufunika ndalama zoti zigwire ntchito yokagawa makondomu m’madera ovuta kufikako pofuna kuchepetsa kufala kwa kachirombo ka HIV. Izi ndi malingana ndi akuluakulu a bungwe la CSAF omwe amayankhula izi pankumano omwe bungweli linapangitsa ndi atolankhani ochokera nyumba zofalitsa mawu zosiyanasiyana m’dziko muno […]
The post Makondomu akafikeso kumadera ovuta kufika, yatelo CSAF appeared first on Malawi 24.