Makampani opanga mafuta ophikira atsitsa mitengo ya mafuta mwezi wamawa

Boma la Malawi kudzera ku unduna wa zamalonda lati makampani onse opanga komaso kugulitsa mafuta ophikira mdziko muno avomera kuti atsitsa mitengo kuyambira pa 1 mwezi wamawa. Izi zadziwika potsatira mkumano omwe boma linapangitsa sabata ino ndi makampani onse opanga komaso kugulitsa mafuta ophikira komwe mbali zonse zokhudzidwa zimagwirizana pa zoyenera kuchita pankhani yofuna kutsitsa […]

The post Makampani opanga mafuta ophikira atsitsa mitengo ya mafuta mwezi wamawa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です