Apolisi m’boma la Chiradzulu akusakasaka anthu omwe apha mai wa zaka 78 zakubadwa, Edina Makhumba. Mbandazi zathawaso ndi foni ya manja tamabatani, Nkhuku folo, zofunda, ufa wachimanga olemera 5 kilogalamu komaso ndalama yokwana K20,000. Mneneri wa apolisi ku Chiradzulu, Cosmas Kagulo, wati izi zachitika m’mudzi wa Iidala m’bomalo. Iwo anapitiliza kunena kuti mwana wa malemuwa […]
The post Mai wa zaka 78 waphedwa mu nyumba yake ku Chiradzulu appeared first on Malawi 24.