Bungwe la Mai Mbambande motsogozedwa ndi Deborah Mbale, lapepesa mkazi wa mpondamatiki Thom Mpinganjira, mayi Triephornia kamba kosabwera poyera ndi kunena kuti mkazi okwatiwa mkumbuyo komweyu anapeleka 2.5 miliyoni kwacha pa nthawi yomwe bungweli limapemphetsa ndalama. Mayi Mpinganjira anabwera poyera ndikudzudzula utsogoleri wa bungwe la Mai Mbambande kamba kopitiliza kupemphetsabe ndalama yokwana K800,000 pomwe iwo […]
The post Mai Mbambande yapepesa: Yaletsa anthu kusonkha ndalama yokabweza kwa mayi Mpinganjira appeared first on Malawi 24.