Magetsi mpwechemphweche ku Tanzania mpaka achita kuthimitsira matchini

Pena ngati upemphe kwa a neba kuti mwina angotibwerekako wawo, ife tiwapatse wathu. Chifukwa zimene likuchita dziko la Tanzania ndiye eee ndi zodabwitsa. Patangopita masiku pa makina a intaneti dzikoli litadya wani ndi sitima za makono, lero dziko la Tanzania lalengeza kuti layamba lathimitsa makina asanu opanga magetsi chifukwa amasowa kopita nawo. Malinga ndi malipoti […]

The post Magetsi mpwechemphweche ku Tanzania mpaka achita kuthimitsira matchini appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください