Chipatala cha qMzimba chikumagwiritsa ntchito ndalama zosaposera K800,00 pa tsiku kugula mafuta a jenereta kamba ka vuto lakuthimathima kwa magetsi pachipatalachi. Malawi24 yapeza kuti chipatala cha chachikulu cha boma la Mzimba chikumagula malita a pakati pa 250 ndi 300 pa tsiku oyatsila jenereta. Mwachitsanzo, pakati pa 30, December 2023 mpaka pa 1, January, 2024, chipatalachi […]
The post Magetsi avuta pa chipatala cha Mzimba appeared first on Malawi 24.