Mizere yonse mukuyionayi, ati mukuyiona komaliza. Kuyambira lolemba lomweli ili, mafuta akhala paliponse moti malo omwetsera mafuta azichita kuyitanira anthu. Atelo ndi a boma. Malinga ndi mlangizi wa a Chakwera a Ephraim Chibvunde, mafuta osowa pokhala akubwera mu dziko muno ndipo zogona pomwetsera mafuta zitha. A Chibvunde auza nyumba youlutsa mauthenga ya Times kuti anthu […]
The post Mafuta ngambwingambwi akubwera lolemba lomweli – atero a boma appeared first on Malawi 24.