Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima dzulo anayankhula ndi a Malawi ku Mzuzu dzulo komwe anapereka miyambi. A Chilima anafika mu mzindawu dzulo pa ndege ndipo analandilidwa ndi chikhamu cha anthu chomwe chinasonkhana pa pafupi ndi Mzuzu Shoprite. Mu mawu awo a Chilima anapeleka miyambi iwir. Oyamba ndi oti “Moto okonza pa […]
The post Madzi okhalitsa amanunkha — Chilima appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 
