Madotolo konzekani: Boma lilemba anthu ogwira ntchito m’zipatala oposera 5, 000

Pamene boma likukonzekera kulemba anthu ogwira ntchito mzipatala zaboma oposera 5,000, mkulu yemwe amayankhulapo pa nkhani za umoyo wayamikira boma la a Lazarus Chakwera kamba kochita chothekera poonetsa kuti anthuwa alembedwe ntchito. Vuto lakuchepa kwa anthu ogwira mzipatala mdziko lino ndi mwa limodzi lomwe likulowetsa pansi ntchito za umoyo mdziko muno kotero a George Jobe […]

The post Madotolo konzekani: Boma lilemba anthu ogwira ntchito m’zipatala oposera 5, 000 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください