Madotolo adandaula ndi kuchuluka kwa mankhwala a zitsamba pamsika

Gulu la madotolo mdziko muno la Society of Medical Doctors (SMD) ladandaula ndi kuchuluka kwa mankhwala a zitsamba m’misika ya mdziko muno zomwe lati zikukolezera matenda ena pakati pa anthu. Izi ndi malingana ndi mtsogoleri wa gulu SMD Dr Victor Mithi omwe amayankhula ndi imodzi mwa nyumba zofalitsira mawu mdziko muno ndipo anati izi zikusokoneza […]

The post Madotolo adandaula ndi kuchuluka kwa mankhwala a zitsamba pamsika appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です