Unduna owona za chilengedwe ndi kusintha kwa nyengo, mogwirizana ndi nthambi yowana za zanyengo, wati pali chiopsyezo choti sabata ino madera ena m’dziko muno makamaka mchigawo cha kum’mwera kukhala madzi osefukira. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe undunawu komaso bungwe la MET latulutsa Lachitatu pa 27 December, 2023 yomwe ikufotokoza za chiopsyezochi chomwe akuti ndi […]
The post Madera ena kukhala madzi osefukira sabata ino – yatelo MET appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
