MACRA yalamula mawailesi omwe amanenelera mpira uku wakunja kuti azikhala ndi chilolezo

Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) yalamula kuti nyumba zowulutsa mawu zomwe zimanenerera mpira pomwe zikuonera mmakanena akunja kapena a m’dziko muno zikuyenera kupereka umboni kuti zili ndi chilolezo chochita izi pasanathe masiku asanu ndi awiri kuchokera pa 5 February chaka chino. Malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa ndipo yasainidwa ndi mkulu wa bungweli […]

The post MACRA yalamula mawailesi omwe amanenelera mpira uku wakunja kuti azikhala ndi chilolezo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください