Wapampando wa mabungwe omwe asali aboma ku Mzimba a Christopher Melele ati ndiwokhuzidwa kwambiri kuti adindo ena akulephera ntchito m’bomali. Iwo adzudzula zomwe zikuchitika kuti apolisi ya Jenda akukanika kukwizinga mwana wa Inkhosi Khosolo wazaka 25 zakubadwa komanso yemwe ndiwogwira ntchito m’boma, pomwe maumboni woti munthuyo anakwatira msikana wachichepera wazaka 15,ulipo. Melele wati sakuwona chifukwa […]
The post Mabungwe ati apolisi kwa Jenda agwire ntchito mosaona nkhope appeared first on Malawi 24.