Maanja 28 ali kakasi kamba kamvula ya mphamvu yomwe yawononga katundu osiyanasiyana

Maanja okwana 28 akusowa mtengo ogwira kamba ka mvula ya mphamvu yomwe yawononga nyumba komanso katundu osiyanasiyana kwa gulupu Mawawa, mfumu yayikulu Chulu m’boma la Kasungu. Mwakatundu wina wawonongeka kamba ka mvula ya mphamvuyi ndi monga feteleza, mbewu, chimanga, ufa komanso nyumba  zomwe zagwa ndikusasuka madenga. Malingana ndi anthu ena omwe akhudzika ndi mvula yamphamvuyi, […]

The post Maanja 28 ali kakasi kamba kamvula ya mphamvu yomwe yawononga katundu osiyanasiyana appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください