Unduna wa zaulimi wati ukupitiliza kukwanilitsa masomphenya a pulezidenti Lazarus Chakwera oonetsetsa kuti njala itheretu mdziko muno polima zakudya kudzela mu ulimi othilira. Izi anena ndi nduna ya za ulimi a Sam Kawale lero atayendera mmene ntchito yokonzaso Mlambe Mega Farm ikuyendela ku Nkopola, Mangochi. “Mega Farm imeneyi ndi ya ma hekita 800 ndipo ma […]
The post Ma Mega Farm ayambikadi: Kawale akhutisidwa ndi kupita patsogolo kwa Mlambe Mega Farm ku Mangochi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.
Moni Malawi 